Salimo 120:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi iwe lilime lachinyengo,+Munthu adzakupatsa chiyani ndipo adzawonjezera chiyani pa iwe?