2 Samueli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu. 2 Samueli 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Amasa sanachenjere ndi lupanga limene linali m’manja mwa Yowabu. Choncho Yowabuyo anamubaya+ nalo m’mimba ndipo matumbo ake anakhuthukira pansi, moti sanachite kumubaya kawiri. Chotero Amasa anafa. Pamenepo Yowabu ndi Abisai m’bale wake anathamangitsa Sheba mwana wa Bikiri. Salimo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa komanso anthu amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo+ koma m’mitima yawo muli zinthu zoipa.+
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu.
10 Koma Amasa sanachenjere ndi lupanga limene linali m’manja mwa Yowabu. Choncho Yowabuyo anamubaya+ nalo m’mimba ndipo matumbo ake anakhuthukira pansi, moti sanachite kumubaya kawiri. Chotero Amasa anafa. Pamenepo Yowabu ndi Abisai m’bale wake anathamangitsa Sheba mwana wa Bikiri.
3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa komanso anthu amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo+ koma m’mitima yawo muli zinthu zoipa.+