Numeri 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.” Salimo 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musachotse moyo wanga pamodzi ndi anthu ochimwa,+Kapena pamodzi ndi anthu a mlandu wamagazi.+
26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.”