Ekisodo 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Usatsatire khamu pochita zoipa.+ Pa mlandu usapereke umboni wopotoza chilungamo potsatira khamu la anthu.+
2 Usatsatire khamu pochita zoipa.+ Pa mlandu usapereke umboni wopotoza chilungamo potsatira khamu la anthu.+