Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 52:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Lilime lako limakonza chiwembu, ndipo ndi lakuthwa ngati lezala,+

      Limachita zachinyengo.+

  • Salimo 55:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+

      Koma mtima wake umakonda ndewu.+

      Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+

      Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+

  • Salimo 64:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+

      Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+

  • Miyambo 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Munthu wonenera mnzake umboni wonama ali ngati chibonga cha kunkhondo, lupanga, ndi muvi wakuthwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena