Salimo 50:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Walekerera pakamwa pako kulankhula zinthu zoipa,+Ndipo ukugwiritsa ntchito lilime lako kulankhula zachinyengo.+ Salimo 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+ Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+ Salimo 64:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+
19 Walekerera pakamwa pako kulankhula zinthu zoipa,+Ndipo ukugwiritsa ntchito lilime lako kulankhula zachinyengo.+
4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+
7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+