Salimo 52:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Umakonda kwambiri zinthu zoipa kuposa zabwino,+Umakonda kwambiri kulankhula chinyengo kuposa kulankhula chilungamo.+ [Seʹlah.] Yeremiya 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense amapusitsa mnzake+ ndipo salankhula choonadi ngakhale pang’ono. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo adzitopetsa okha ndi kuchita zinthu zoipa.+
3 Umakonda kwambiri zinthu zoipa kuposa zabwino,+Umakonda kwambiri kulankhula chinyengo kuposa kulankhula chilungamo.+ [Seʹlah.]
5 Aliyense amapusitsa mnzake+ ndipo salankhula choonadi ngakhale pang’ono. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo adzitopetsa okha ndi kuchita zinthu zoipa.+