Salimo 50:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Walekerera pakamwa pako kulankhula zinthu zoipa,+Ndipo ukugwiritsa ntchito lilime lako kulankhula zachinyengo.+ Mika 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+
19 Walekerera pakamwa pako kulankhula zinthu zoipa,+Ndipo ukugwiritsa ntchito lilime lako kulankhula zachinyengo.+
12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+