Yesaya 59:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti m’manja mwanu mwaipitsidwa ndi magazi,+ ndipo zala zanu zaipitsidwa ndi zolakwa.+ Milomo yanu yanena zabodza. Lilime lanu limangokhalira kunena zinthu zopanda chilungamo.+ Mika 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+
3 Pakuti m’manja mwanu mwaipitsidwa ndi magazi,+ ndipo zala zanu zaipitsidwa ndi zolakwa.+ Milomo yanu yanena zabodza. Lilime lanu limangokhalira kunena zinthu zopanda chilungamo.+
2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+