Salimo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu. Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+ Yesaya 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Wolungama wawonongedwa,+ koma palibe amene zikum’khudza.+ Anthu amene amasonyeza kukoma mtima kosatha akusonkhanitsidwira kwa akufa+ popanda wozindikira kuti munthu wolungamayo wafa ndipo wathawa tsoka.+ Aroma 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Palibe munthu wolungama ndi mmodzi yemwe.+
12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu.
14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+
57 Wolungama wawonongedwa,+ koma palibe amene zikum’khudza.+ Anthu amene amasonyeza kukoma mtima kosatha akusonkhanitsidwira kwa akufa+ popanda wozindikira kuti munthu wolungamayo wafa ndipo wathawa tsoka.+