Hoseya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumtima mwawo saganiza+ kuti ine ndidzakumbukira zochita zawo zonse zoipa.+ Tsopano ntchito zawo zawazungulira+ ndipo zili pamaso panga.+ Mika 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+
2 Mumtima mwawo saganiza+ kuti ine ndidzakumbukira zochita zawo zonse zoipa.+ Tsopano ntchito zawo zawazungulira+ ndipo zili pamaso panga.+
12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+