Yeremiya 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ponena za anthu awa Yehova wati: “Iwo akukonda kuyendayenda+ ndipo sanalamulire mapazi awo.+ Choncho Yehova sakukondwera nawo,+ moti adzakumbukira zolakwa zawo ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.”+ Amosi 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+
10 Ponena za anthu awa Yehova wati: “Iwo akukonda kuyendayenda+ ndipo sanalamulire mapazi awo.+ Choncho Yehova sakukondwera nawo,+ moti adzakumbukira zolakwa zawo ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.”+
7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+