Deuteronomo 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+ Salimo 47:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzatisankhira cholowa,+Chimene Yakobo, amene amamukonda, anakondwera nacho.+ [Seʹlah.] Salimo 68:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+Iye akulamulira Isiraeli ndipo mphamvu zake zili m’mitambo.+
26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+
34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+Iye akulamulira Isiraeli ndipo mphamvu zake zili m’mitambo.+