Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Malaki 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+ Koma inu mwanena kuti: “Mumatikonda motani?”+ “Kodi Esau sanali m’bale wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,”+ watero Yehova.
6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+
2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+ Koma inu mwanena kuti: “Mumatikonda motani?”+ “Kodi Esau sanali m’bale wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,”+ watero Yehova.