Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake. Deuteronomo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+ Yesaya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha.
15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.
5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+
2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha.