2 Samueli 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+ Salimo 89:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+ Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+
47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+
26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+
95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+