Salimo 18:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wa chipulumutso changa akhale wokwezeka.+ Salimo 89:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+
26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+