Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake. 2 Samueli 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+ Salimo 98:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+
15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.
47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+
4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+