Hoseya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Isiraeli wakhala wamakani* ngati ng’ombe yamakani.+ Choncho kodi Yehova angawawete ngati nkhosa yamphongo yaing’ono pamalo otakasuka?
16 Isiraeli wakhala wamakani* ngati ng’ombe yamakani.+ Choncho kodi Yehova angawawete ngati nkhosa yamphongo yaing’ono pamalo otakasuka?