Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 31:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pakuti ndidzawalowetsa m’dziko limene ndinalumbirira makolo awo,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Kumeneko iwo adzadya+ ndi kukhuta, ndipo adzatukuka+ ndi kutembenukira kwa milungu ina.+ Adzatumikira milungu imeneyo ndi kundichitira chipongwe, ndipo adzaphwanya pangano langa.+

  • Nehemiya 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iwo analanda mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Analandanso nthaka yachonde,+ nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino,+ zitsime,*+ minda ya mpesa ndi ya maolivi+ ndi mitengo ya zipatso yochuluka. Atatero, anayamba kudya, kukhuta,+ kunenepa+ ndi kukondwera ndi ubwino wanu waukulu.+

  • Salimo 73:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Diso lawo latuzuka chifukwa cha kunenepa.+

      Achita zambiri kuposa zolingalira za mtima wawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena