Levitiko 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Dzikolo lidzakupatsani zipatso zake.+ Mudzadya ndi kukhuta, ndipo mudzakhala otetezeka mmenemo.+ Deuteronomo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Mukadzadya ndi kukhuta+ mudzatamandenso+ Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha dziko labwino limene wakupatsani.+ Hoseya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+
10 “Mukadzadya ndi kukhuta+ mudzatamandenso+ Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha dziko labwino limene wakupatsani.+
6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+