Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+

  • Salimo 67:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Dziko lapansi lidzapereka zipatso zake.+

      Mulungu, ndithu Mulungu wathu, adzatidalitsa.+

  • Ezekieli 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mtengo wam’munda udzabereka zipatso.+ Nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala m’dziko lawo mwabata.+ Ndikadzathyola goli lawo+ ndi kuwapulumutsa m’dzanja la amene anali kuwagwiritsa ntchito monga akapolo,+ adzadziwa kuti ine ndine Yehova.

  • Yoweli 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Malo opunthira mbewu adzadzaza ndi mbewu zopunthidwa ndipo malo ogweramo vinyo watsopano ndi mafuta adzasefukira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena