Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Muzisunga malangizo anga ndi zigamulo zanga. Mukatero mudzakhala otetezeka m’dzikolo.+

  • Miyambo 1:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Koma munthu wondimvera adzakhala mwabata+ ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+

  • Yeremiya 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena