Salimo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Moyo wake udzasangalala ndi ubwino wa Mulungu,+Mbadwa zake zidzatenga dziko lapansi kukhala lawo.+ Yesaya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+ Chivumbulutso 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza unasunga mawu onena za kupirira kwanga,+ inenso ndidzakusunga+ pa ola la kuyesedwa, limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakusunga pa ola limene likubwera kudzayesa okhala padziko lapansi.+
13 Moyo wake udzasangalala ndi ubwino wa Mulungu,+Mbadwa zake zidzatenga dziko lapansi kukhala lawo.+
18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+
10 Popeza unasunga mawu onena za kupirira kwanga,+ inenso ndidzakusunga+ pa ola la kuyesedwa, limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakusunga pa ola limene likubwera kudzayesa okhala padziko lapansi.+