Deuteronomo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho muwoloke Yorodano+ ndi kukhala m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu.+ Iye adzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhaladi otetezeka.+ Salimo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzagona pansi ndi kupeza tulo mu mtendere,+Pakuti inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+ Miyambo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma munthu wondimvera adzakhala mwabata+ ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+
10 Choncho muwoloke Yorodano+ ndi kukhala m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu.+ Iye adzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhaladi otetezeka.+
8 Ndidzagona pansi ndi kupeza tulo mu mtendere,+Pakuti inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+