Levitiko 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzisunga malangizo anga ndi zigamulo zanga. Mukatero mudzakhala otetezeka m’dzikolo.+ Deuteronomo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho muwoloke Yorodano+ ndi kukhala m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu.+ Iye adzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhaladi otetezeka.+ Ezekieli 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘“Ine ndidzachita nazo pangano la mtendere.+ Ndidzachotsa zilombo zolusa zakutchire m’dzikomo.+ Nkhosazo zidzakhala m’chipululu popanda choziopsa ndipo zizidzagona m’nkhalango.+
10 Choncho muwoloke Yorodano+ ndi kukhala m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu.+ Iye adzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhaladi otetezeka.+
25 “‘“Ine ndidzachita nazo pangano la mtendere.+ Ndidzachotsa zilombo zolusa zakutchire m’dzikomo.+ Nkhosazo zidzakhala m’chipululu popanda choziopsa ndipo zizidzagona m’nkhalango.+