Deuteronomo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ineyo ndifera m’dziko lino.+ Sindiwoloka Yorodano, koma inu muwoloka ndi kutenga dziko labwinoli. Deuteronomo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa m’dziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+
9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa m’dziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+