Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Anachita izi kuti achotse mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, ndi kulowetsamo inu, kukupatsani dziko lawo kuti likhale cholowa chanu monga mmene zilili lero.+

  • Deuteronomo 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako,+ adzakuchotsera mitundu ikuluikulu.+ Adzakuchotsera Ahiti,+ Agirigasi,+ Aamori,+ Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi+ ndi Ayebusi,+ mitundu 7 ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa iwe.+

  • Deuteronomo 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova adzachotsa mitundu yonseyi chifukwa cha inu,+ ndipo mitundu yamphamvu ndi yaikulu kuposa inu mudzailanda dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena