Deuteronomo 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti mukuwoloka Yorodano ndi kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala lanu. Mukalitengedi ndi kukhala momwemo.+ Yoswa 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko.
31 Pakuti mukuwoloka Yorodano ndi kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala lanu. Mukalitengedi ndi kukhala momwemo.+
19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko.