Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’”

  • Yoswa 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachotsa chitonzo cha Iguputo pa inu.”+ Chotero malowo anayamba kuwatchula kuti Giligala,+ kufikira lero.

  • Yoswa 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Amuna a ku Gibeoni ataona zimenezi, anatumiza uthenga kwa Yoswa kumsasa ku Giligala,+ kuti: “Musatitaye ife akapolo anu!+ Bwerani kuno msanga, mudzatithandize ndi kutipulumutsa. Mafumu onse a Aamori okhala kudera lamapiri atisonkhanira kuti atithire nkhondo.”

  • Mika 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu anthu anga, chonde kumbukirani+ zimene Balaki mfumu ya Mowabu anakonza kuti achite+ ndiponso zimene Balamu mwana wa Beori anamuyankha.+ Kumbukirani zimene zinachitika kuyambira ku Sitimu+ kukafika ku Giligala.+ Zimenezo zinachitika n’cholinga chakuti zochita za Yehova zolungama zidziwike.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena