Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+ Aefeso 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero nthawi zonse muzikumbukira kuti poyamba munali anthu a mitundu ina mwakuthupi.+ Anthu otchedwa “odulidwa,” amene anadulidwa mwakuthupi ndi manja,+ anali kukutchani “osadulidwa.”
7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+
11 Chotero nthawi zonse muzikumbukira kuti poyamba munali anthu a mitundu ina mwakuthupi.+ Anthu otchedwa “odulidwa,” amene anadulidwa mwakuthupi ndi manja,+ anali kukutchani “osadulidwa.”