Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Kuwonjezera apo, pa Tabera,+ pa Masa+ ndi pa Kibiroti-hatava+ munaputanso mkwiyo wa Yehova.+ Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo analitu kumupandukira kawirikawiri m’chipululu,+Anali kumukhumudwitsa m’chipululumo!+ Aheberi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+
16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+