Yesaya 63:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+ Aefeso 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene mwaikidwa chidindo chake,+ cha pa tsiku limene mudzamasulidwa ndi dipo.+ Aheberi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+
10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+
30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene mwaikidwa chidindo chake,+ cha pa tsiku limene mudzamasulidwa ndi dipo.+
16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+