Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo analitu kumupandukira kawirikawiri m’chipululu,+Anali kumukhumudwitsa m’chipululumo!+ Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+ Aefeso 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene mwaikidwa chidindo chake,+ cha pa tsiku limene mudzamasulidwa ndi dipo.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene mwaikidwa chidindo chake,+ cha pa tsiku limene mudzamasulidwa ndi dipo.+