Levitiko 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo. Deuteronomo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mitima yanu muichite mdulidwe+ ndipo musakhalenso ouma khosi.+
41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo.