1 Mafumu 8:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndiyeno iwo n’kuzindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo+ n’kulapa,+ ndipo akapempha+ chifundo kwa inu m’dziko la adani awo amene awagwira,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+ 2 Mbiri 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuwonjezera apo, Nebukadinezara anagwira anthu amene sanaphedwe ndi lupanga ndipo anawatenga kupita nawo ku Babulo.+ Anthuwo anakakhala antchito+ ake ndi a ana ake kufikira pamene ufumu wa Perisiya+ unayamba kulamulira.
47 ndiyeno iwo n’kuzindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo+ n’kulapa,+ ndipo akapempha+ chifundo kwa inu m’dziko la adani awo amene awagwira,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+
20 Kuwonjezera apo, Nebukadinezara anagwira anthu amene sanaphedwe ndi lupanga ndipo anawatenga kupita nawo ku Babulo.+ Anthuwo anakakhala antchito+ ake ndi a ana ake kufikira pamene ufumu wa Perisiya+ unayamba kulamulira.