Numeri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+ Numeri 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Malo amenewo anawatcha Kibiroti-hatava,+ chifukwa anafotserapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+
4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+
34 Malo amenewo anawatcha Kibiroti-hatava,+ chifukwa anafotserapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+