Numeri 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pake ananyamuka m’chipululu cha Sinai, n’kukamanga msasa ku Kibiroti-hatava.+ Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Kuwonjezera apo, pa Tabera,+ pa Masa+ ndi pa Kibiroti-hatava+ munaputanso mkwiyo wa Yehova.+