Numeri 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Malo amenewo anawatcha Kibiroti-hatava,+ chifukwa anafotserapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+ Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Kuwonjezera apo, pa Tabera,+ pa Masa+ ndi pa Kibiroti-hatava+ munaputanso mkwiyo wa Yehova.+
34 Malo amenewo anawatcha Kibiroti-hatava,+ chifukwa anafotserapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+