Oweruza 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu a anthu ena otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi,+Kumeneko anayamba kusimba ntchito zolungama za Yehova,+Anasimba ntchito zolungama za anthu ake okhala m’midzi ya Isiraeli.Atatero m’pamene anthu a Yehova anapita kumizinda. Salimo 71:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+Padzanena za chipulumutso chanu tsiku lonse,+Pakuti ntchito za chilungamo ndi chipulumutso chanu ndi zochuluka ndipo sindinathe kuziwerenga.+ Aroma 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu anam’pereka monga nsembe yachiyanjanitso,+ mwa kukhala ndi chikhulupiriro m’magazi ake.+ Mulungu anachita izi pofuna kuonetsa chilungamo chake pokhululuka machimo+ amene anachitika kale, pamene iye anali kusonyeza khalidwe losakwiya msanga,+
11 Mawu a anthu ena otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi,+Kumeneko anayamba kusimba ntchito zolungama za Yehova,+Anasimba ntchito zolungama za anthu ake okhala m’midzi ya Isiraeli.Atatero m’pamene anthu a Yehova anapita kumizinda.
15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+Padzanena za chipulumutso chanu tsiku lonse,+Pakuti ntchito za chilungamo ndi chipulumutso chanu ndi zochuluka ndipo sindinathe kuziwerenga.+
25 Mulungu anam’pereka monga nsembe yachiyanjanitso,+ mwa kukhala ndi chikhulupiriro m’magazi ake.+ Mulungu anachita izi pofuna kuonetsa chilungamo chake pokhululuka machimo+ amene anachitika kale, pamene iye anali kusonyeza khalidwe losakwiya msanga,+