Ekisodo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno wansembe+ wa ku Midiyani anali ndi ana aakazi 7. Monga mwa masiku onse, iwo anafika pachitsimepo ndipo anatunga madzi ndi kuwathira m’ngalande kuti ziweto za bambo awo zimwe.+
16 Ndiyeno wansembe+ wa ku Midiyani anali ndi ana aakazi 7. Monga mwa masiku onse, iwo anafika pachitsimepo ndipo anatunga madzi ndi kuwathira m’ngalande kuti ziweto za bambo awo zimwe.+