Genesis 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo+ mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira.
20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo+ mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira.