Miyambo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amakhala wokonzeka kugwira ntchito yolimba, ndipo amalimbitsa manja ake.+ Miyambo 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 M’patseni zipatso za manja ake,+ ndipo ntchito zake zimutamande ngakhale m’zipata.+