Genesis 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Abulahamu anathamangira kwa Sara n’kumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu ya seya,* uukande, ndipo upange makeke ozungulira.”+ Genesis 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo+ mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira.
6 Chotero Abulahamu anathamangira kwa Sara n’kumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu ya seya,* uukande, ndipo upange makeke ozungulira.”+
20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo+ mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira.