-
Ekisodo 12:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Ndiyeno ufa wokanda umene anachoka nawo ku Iguputo uja anayamba kuuphika mikate yozungulira yopanda chofufumitsa, chifukwa ufa wokandawo unalibe zofufumitsa. Ufawo unalibe zofufumitsa chifukwa chakuti anawapitikitsa ku Iguputo ndipo anachoka mofulumira kwambiri. Komanso iwo anaphika mikateyo chifukwa chakuti sanathe kukonza chakudya chilichonse ponyamuka.+
-