Ekisodo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tsopano uona zimene ndichite kwa Farao.+ Chifukwa cha dzanja lamphamvu, iye awalola kuchoka, ndipo chifukwa cha dzanja lamphamvu awatulutsa m’dziko lake.”+ Ekisodo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Patsala mliri umodzi wokha woti ndikanthe nawo Farao ndi Iguputo. Kenako adzakulolani kuchoka m’dziko lino.+ Pokulolani kuchoka ndi zonse zimene muli nazo, adzachita kukupitikitsani.+ Ekisodo 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nthawi yomweyo Farao anaitanitsa+ Mose ndi Aroni usiku, ndipo anati: “Nyamukani, chokani pakati pa anthu anga, inuyo ndi ana onse a Isiraeli. Pitani, katumikireni Yehova, monga momwe mwanenera.+
6 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tsopano uona zimene ndichite kwa Farao.+ Chifukwa cha dzanja lamphamvu, iye awalola kuchoka, ndipo chifukwa cha dzanja lamphamvu awatulutsa m’dziko lake.”+
11 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Patsala mliri umodzi wokha woti ndikanthe nawo Farao ndi Iguputo. Kenako adzakulolani kuchoka m’dziko lino.+ Pokulolani kuchoka ndi zonse zimene muli nazo, adzachita kukupitikitsani.+
31 Nthawi yomweyo Farao anaitanitsa+ Mose ndi Aroni usiku, ndipo anati: “Nyamukani, chokani pakati pa anthu anga, inuyo ndi ana onse a Isiraeli. Pitani, katumikireni Yehova, monga momwe mwanenera.+