Ekisodo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+ Ekisodo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tengani nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu monga mwanenera,+ ndipo pitani. Komanso mukandipemphere madalitso.”
20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+
32 Tengani nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu monga mwanenera,+ ndipo pitani. Komanso mukandipemphere madalitso.”