Ekisodo 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero pakati pa usiku, Yehova anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo.+ Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene wakhala pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa mkaidi amene ali m’ndende yapansi, ndiponso mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse.+ Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+ Salimo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova wanena kuti: “Chifukwa cha kuponderezedwa kwa osautsika, chifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka pa nthawiyo,+Ndidzawateteza kwa aliyense wowanyodola.”+
29 Chotero pakati pa usiku, Yehova anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo.+ Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene wakhala pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa mkaidi amene ali m’ndende yapansi, ndiponso mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse.+
13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+
5 Tsopano Yehova wanena kuti: “Chifukwa cha kuponderezedwa kwa osautsika, chifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka pa nthawiyo,+Ndidzawateteza kwa aliyense wowanyodola.”+