Genesis 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abulahamu anatenga mafuta a mkaka, mkaka, ndi ng’ombe yaing’ono yamphongo imene anakonza ija, n’kukaziika pamene panali alendowo.+ Pamene iwo anali kudya atakhala pansi pa mtengo, iye anaimirira chapafupi.+ 2 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita ndipo anapita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba+ a Asiriya sanabwerenso ku Isiraeli.
8 Ndiyeno Abulahamu anatenga mafuta a mkaka, mkaka, ndi ng’ombe yaing’ono yamphongo imene anakonza ija, n’kukaziika pamene panali alendowo.+ Pamene iwo anali kudya atakhala pansi pa mtengo, iye anaimirira chapafupi.+
23 Chotero mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita ndipo anapita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba+ a Asiriya sanabwerenso ku Isiraeli.