Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma mwamuna wokalamba uja anati: “Mtendere ukhale nawe!+ Ine ndidzakupatsa chilichonse chimene ungafunikire.+ Koma usagone pabwalo la mzinda.”

  • Luka 24:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma iwo anamuumiriza kuti: “Tiyeni tikhalebe limodzi, chifukwa kunja kwayamba kuda ndipo tsiku latha kale.” Pamenepo analowa ndi kukakhala nawo.

  • Machitidwe 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena